12 Pamenepo anabwera ku Yerusalemu kucokera ku phiri lonenedwa la Azitona, limene liyandikana ndi Yerusalemu, loyendako tsiku la Sabata.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 1
Onani Macitidwe 1:12 nkhani