14 Iwo onse analikukangalika m'kupemphera, pamodzi ndi akazi, ndi Mariya, amace wa Yesu, ndi abale ace omwe.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 1
Onani Macitidwe 1:14 nkhani