15 Ndipo m'masiku awa anaimirira Petro pakati pa abale, nati (gulu la anthu losonkhana pamalo pomwe ndilo ngati zana limodzi ndi makumi awiri),
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 1
Onani Macitidwe 1:15 nkhani