18 (Uyutu tsono anadzitengera kadziko ndi mphoto ya cosalungama; ndipo anagwa camutu, naphulika pakati, ndi matumbo ace onse anakhuthuka;
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 1
Onani Macitidwe 1:18 nkhani