19 ndipo cinadziwika ndi onse akukhala ku Yerusalemu; kotero kuti m'manenedwe ao kadzikoka kanachedwa Akeldama, ndiko, kadziko ka mwazi.)
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 1
Onani Macitidwe 1:19 nkhani