21 Ndipo Petro anatsikira kwa anthuwo, nati, Taonani, ine ndine amene mumfuna; cifukwa cace mwadzera nciani?
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 10
Onani Macitidwe 10:21 nkhani