3 Iye anapenya m'masomphenya poyera, mngelo wa Mulungu alinkudza kwa iye, ngati ora lacisanu ndi cinai la usana, nanena naye, Komeliyo.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 10
Onani Macitidwe 10:3 nkhani