4 Ndipo pompenyetsetsa iye ndi kuopa, anati, Nciani, Mbuye? Ndipo anati kwa iye, Mapemphero ako ndi zacifundo zako zinakwera zikhala cikumbutso pamaso pa Mulungu.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 10
Onani Macitidwe 10:4 nkhani