32 Cifukwa cace tumiza anthu ku Yopa, akaitane Simoni amene anenedwanso Petro; amene acerezedwa m'nyumba ya Simoni wofufuta zikopa, m'mbali mwa nyanja.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 10
Onani Macitidwe 10:32 nkhani