33 Pamenepo ndinatumiza kwa inu osacedwa; ndipo mwacita bwino mwadza kuno, Cifukwa cace taonani tiri tonse pano pamaso pa Mulungu, kumva zonse Ambuye anakulamulirani.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 10
Onani Macitidwe 10:33 nkhani