42 Ndipo 2 anatilamulira ife tilalikire kwa anthu, ndipo ticite umboni kuti 3 Uyu ndiye amene aikidwa ndi Mulungu akhale woweruza amoyo ndi akufa.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 10
Onani Macitidwe 10:42 nkhani