43 4 Ameneyu aneneri onse amcitira umboni, kuti onse akumkhulupirira iye adzalandira cikhululukiro ca macimo ao, mwa dzina lace.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 10
Onani Macitidwe 10:43 nkhani