Macitidwe 11:5 BL92

5 Ndinali ine m'mudzi wa Yopa ndi kupemphera; ndipo m'kukomoka ndinaona masomphenya, cotengera cirikutsika, ngati cinsaru cacikuru cogwiridwa pa ngondya zace zinai; ndi kutsika kumwamba, ndipo cinadza pali ine;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 11

Onani Macitidwe 11:5 nkhani