Macitidwe 11:6 BL92

6 cimeneco ndidacipenyetsetsa ndinacilingirira, ndipo ndinaona nyama za miyendo inai za padziko ndi zirombo, ndi zokwawa, ndi mbalame za m'mlengalenga.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 11

Onani Macitidwe 11:6 nkhani