13 Ndipo m'mene anagogoda pa citseko ca pakhomo, linadza kudzabvomera buthu, dzina lace Roda.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 12
Onani Macitidwe 12:13 nkhani