14 Ndipo pozindikira mau ace a Petro, cifukwa ca kukondwera sanatsegula pakhomo, koma anathamanga nalowanso, nawauza kuti Petro alikuima pakhomo.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 12
Onani Macitidwe 12:14 nkhani