1 Ndipo anafikanso ku Derbe ndi Lustra; ndipo taonani, panali wophunzira wina pamenepo, dzina lace Timoteo, amace ndiye Myuda wokhulupira; koma atate wace ndiye Mhelene.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 16
Onani Macitidwe 16:1 nkhani