Macitidwe 16:38 BL92

38 Ndipo akapitao anafotokozera mauwo kwa oweruza; ndipo iwowo anaopa, pakumva kuti anali Aroma.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 16

Onani Macitidwe 16:38 nkhani