Macitidwe 16:37 BL92

37 Koma Paulo anati kwa iwo, Adatikwapula ire pamaso pa anthu, osamva mlandu wathu, ire amene tiri Aroma, natiika m'ndende; ndipo tsopano kodi afuna kutiturutsira ire m'tseri? Iai, ndithu; koma adze okha atiturutse.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 16

Onani Macitidwe 16:37 nkhani