Macitidwe 16:36 BL92

36 Ndipo mdindo anafotokozera mauwo kwa Paulo, nati, Oweruza atumiza mau kunena kuti mumuke; tsopanotu turukani, mukani mumtendere.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 16

Onani Macitidwe 16:36 nkhani