Macitidwe 17:32 BL92

32 Ndipo pamene anamva za kuuka kwa akufa ena anaseka pwepwete; koma ena anati, Tidzakumvanso za cimeneci.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 17

Onani Macitidwe 17:32 nkhani