31 cifukwa anapangira tsiku limene adzaweruza dziko lokhalamo anthu m'cilungamo, ndi munthu amene anamuikiratu; napatsa anthu onse citsimikizo, pamene anamuukitsa iye kwa akufa.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 17
Onani Macitidwe 17:31 nkhani