4 Ndipo ena a iwo anakopedwa, nadziphatika kwa Paulo ndi Sila; ndi Ahelene akupembedza aunyinji ndithu, ndi akazi akuru osati owerengeka.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 17
Onani Macitidwe 17:4 nkhani