5 Koma pamene Sila ndi Timoteo anadza potsika ku Makedoniya, Paulo anapsinjidwa ndi mau, nacitira umboni kwa Ayuda kuti Yesu ndiye Kristu.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 18
Onani Macitidwe 18:5 nkhani