6 Koma pamene iwo anamkana, nacita mwano, anakutumula maraya ace, nati kwa iwo, Mwazi wanu ukhale pa mitu yanu; ine ndiribe kanthu; kuyambira tsopano ndinka kwa amitundu.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 18
Onani Macitidwe 18:6 nkhani