Macitidwe 19:12 BL92

12 kotero kuti anamuka nazo kwa odwala nsaru zopukutira ndi za panchito, zocokera pathupi pace, ndipo nthenda zinawacokera, ndi mizimu yoipa inaturuka.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 19

Onani Macitidwe 19:12 nkhani