Macitidwe 19:13 BL92

13 Koma Ayuda enanso oyendayenda, oturutsa ziwanda, anadziyesa kuchula pa iwo amene anali ndi mizimu yoipa dzina la Ambuye Yesu, kuti, Ndikulumbirirani pa Yesu amene amlalika Paulo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 19

Onani Macitidwe 19:13 nkhani