Macitidwe 19:33 BL92

33 Ndipo anaturutsa Alesandro m'khamumo, kumturutsa iye Ayuda. Ndipo Alesandro anatambasula dzanja, nafuna kudzikanira kwa anthu adasonkhanawo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 19

Onani Macitidwe 19:33 nkhani