34 Koma pozindikira kuti ali Myuda, kunali mau amodzi a kwa onse akupfuula monga maora awiri, Wamkuru ndi Artemi wa Aefeso.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 19
Onani Macitidwe 19:34 nkhani