Macitidwe 2:6 BL92

6 Koma pocitika mau awa, unyinji wa anthu unasonkhana, nusokonezedwa, popeza yense anawamva alikulankhula m'cilankhulidwe cace ca iye yekha.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 2

Onani Macitidwe 2:6 nkhani