15 Ndipo m'mene tidacokerapo, m'mawa mwace tinafika pandunjipa Kiyo; ndi m'mawa mwace tinangokoceza ku Samo, ndi m'mawa mwace tinafika ku Mileto.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 20
Onani Macitidwe 20:15 nkhani