16 Pakuti Paulo adatsimikiza mtima apitirire pa Efeso, angataye nthawi m'Asiya; pakuti anafulumira, ngati kutheka, akhale ku Yerusalemu tsiku la Pentekoste.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 20
Onani Macitidwe 20:16 nkhani