1 Ndipo kunali, titalekana nao ndi kukankha ngalawa, tinadza molunjika ku Ko, ndi m'mawa mwace ku Rode, ndipo pocokerapo ku Patara;
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 21
Onani Macitidwe 21:1 nkhani