3 Ndipo pamene tinafika popenyana ndi Kupro, tinacisiya kulamanzere, ntinapita ku Suriya; ndipo tinakoceza ku Turo; pakuti pamenepo ngalawainafuna kutula akatundu ace.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 21
Onani Macitidwe 21:3 nkhani