4 Ndipo m'mene tinapeza ophunzira, tinakhalako masikuasanu ndi awiri; ndipo iwowa ananena ndi Paulo mwa Mzimu, kuti asakwere ku Yerusalemu.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 21
Onani Macitidwe 21:4 nkhani