7 Ndipo ife titatsiriza ulendo wathu wocokera ku Turo, tinafika ku Ptolemayi; ndipo m'mene tidalankhula abale, tinakhala nao tsiku limodzi.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 21
Onani Macitidwe 21:7 nkhani