Macitidwe 22:26 BL92

26 Ndipo pakumva ici kenturiyoyo, ananka kwa kapitao wamkuru, namuuza, nanena, Nciani ici uti ucite? pakuti munthuyo ndiye Mroma.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 22

Onani Macitidwe 22:26 nkhani