Macitidwe 22:25 BL92

25 Ndipo m'mene anammanga iye ndi nsingazo, Paulo anati kwa kenturiyo wakuimirirako, Kodinkuloleka kwa inu kukwapula munthu Mroma, mlandu wace wosamveka?

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 22

Onani Macitidwe 22:25 nkhani