6 Ndipo kunali, pakupita ine ndi kuyandikira ku Damasiko, monga usana, mwadzidzidzi kunandiwalira pondizungulira ine kuunika kwakukuru kocokera kumwamba.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 22
Onani Macitidwe 22:6 nkhani