7 Ndipo ndinagwapansitu, ndipondinamva mau akunena nane, Saulo, Saulo, undilonda-londeranii Ine?
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 22
Onani Macitidwe 22:7 nkhani