20 Ndipo anati, Ayuda anapangana kuti akufunseni mutsike naye Paulo mawa ku bwalo la mirandu, monga ngati mufuna kufunsitsa za iye.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 23
Onani Macitidwe 23:20 nkhani