Macitidwe 23:22 BL92

22 Pamenepo ndipo kapitao wamkuru anauza mnyamatayo apite, namlamulira kuti, Usauze munthu yense kuti wandizindikiritsa izi.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 23

Onani Macitidwe 23:22 nkhani