Macitidwe 23:23 BL92

23 Ndipo anaitana akenturiyo awiri, nati, Mukonzeretu asilikari mazana awiri, apite kufikira Kaisareya, ndi apakavalo makumi asanu ndi awiri, ndi anthungo mazana awiri, acoke ora lacitatu la usiku;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 23

Onani Macitidwe 23:23 nkhani