8 Pakutitu Asaduki anena kuti kulibe kuuka kwa akufa, kapena mngelo, kapena mzimu; koma Afarisi abvomereza ponse pawiri.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 23
Onani Macitidwe 23:8 nkhani