10 Koma Paulo anati, ndirikuimirira pa mpando waciweruziro wa Kaisara, pompano ndiyenera kuweruzidwa ine; Ayuda sindinawacitira-kanthu koipa, monga mudziwanso nokha bwino.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 25
Onani Macitidwe 25:10 nkhani