Macitidwe 25:11 BL92

11 Pamenepo ngati ndiri wocita zoipa, ngati ndacita kanthu kakuyenera imfa, sindikana kufa; koma ngati zinthuzi awa andinenera nazo ziri zacabe, palibe mmodzi akhoza kundipereka kwa iwo. Nditurukira kwa Kaisara.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 25

Onani Macitidwe 25:11 nkhani