Macitidwe 25:24 BL92

24 Ndipo Festo anati, Mfumu Agripa, ndi amuna inu nonse muli nafe pano pamodzi, muona uyu, amene unyinji wonse wa Ayuda anandiuza za iye, ku Yerusalemu ndi kunonso, ndi kupfuula kuti sayeneranso kukhala ndi moyo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 25

Onani Macitidwe 25:24 nkhani