25 Koma ndinapeza ine kuti sanacita kanthu, koyenera imfa iye; ndipo popeza, iye yekha anati akaturukire kwa Augusto, ndatsimikiza mtima kumtumizako.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 25
Onani Macitidwe 25:25 nkhani