Macitidwe 3:12 BL92

12 Koma m'mene Petro anaciona, anayankha kwa anthu, Amuna inu a Israyeli, muzizwa naye bwanji ameneyo? kapena mutipenyetsetsa ife bwanji, monga ngati tamyendetsa iye ndi mphamvu ya ife eni, kapena ndi cipembedzo cathu?

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 3

Onani Macitidwe 3:12 nkhani