Macitidwe 4:7 BL92

7 Ndipo m'mene anawaimika pakati, anafunsa kuti, Ndi mphamvu yanji, kapena m'dzina lanji, mwacita ici inu?

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 4

Onani Macitidwe 4:7 nkhani